Ezekieli 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Unayamba kuchita uhule ndi ana aamuna a Iguputo,+ anthu a ziwalo zikuluzikulu amene ukukhala nawo pafupi.+ Unapitiriza kuwonjezera uhule wako kuti undikwiyitse. Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+
26 Unayamba kuchita uhule ndi ana aamuna a Iguputo,+ anthu a ziwalo zikuluzikulu amene ukukhala nawo pafupi.+ Unapitiriza kuwonjezera uhule wako kuti undikwiyitse.
4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+