Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+ Aheberi 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso, kodi Mulungu ananyansidwa ndi ndani kwa zaka 40?+ Kodi sananyansidwe ndi anthu amene anachimwa aja, amene anafera m’chipululu?+
29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+
17 Komanso, kodi Mulungu ananyansidwa ndi ndani kwa zaka 40?+ Kodi sananyansidwe ndi anthu amene anachimwa aja, amene anafera m’chipululu?+