Deuteronomo 1:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Motero ine ndinalankhula nanu, ndipo simunamvere koma munayamba kupandukira+ lamulo la Yehova ndi kuchita zinthu modzikuza, motero munanyamuka kupita m’phiri.+ Miyambo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+
43 Motero ine ndinalankhula nanu, ndipo simunamvere koma munayamba kupandukira+ lamulo la Yehova ndi kuchita zinthu modzikuza, motero munanyamuka kupita m’phiri.+