Numeri 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu akachita tchimo mosazindikira, pazikhala lamulo limodzi, kwa mbadwa ya ana a Isiraeli ndi kwa mlendo wokhala pakati pawo.+
29 Munthu akachita tchimo mosazindikira, pazikhala lamulo limodzi, kwa mbadwa ya ana a Isiraeli ndi kwa mlendo wokhala pakati pawo.+