Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa. Muzim’konda mmene mumadzikondera nokha,+ chifukwa inunso munali alendo m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

  • Levitiko 20:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli, ndiponso mlendo aliyense wokhala mu Isiraeli, wopereka mwana wake aliyense kwa Moleki,*+ aziphedwa ndithu. Nzika za m’dziko lanu zizimupha mwa kum’ponya miyala.

  • Levitiko 24:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+

  • Aroma 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kapena kodi iye ndi Mulungu wa Ayuda okha?+ Kodi salinso Mulungu wa anthu a mitundu ina?+ Inde, iye alinso Mulungu wa anthu a mitundu ina,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena