Deuteronomo 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzimanga mphonje m’makona anayi a chovala chako.+ Mateyu 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba+ timene amavala monga zodzitetezera, ndipo amakulitsanso ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa zovala zawo. Luka 8:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mayiyu anamudzera kumbuyo Yesu n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa malaya ake akunja.+ Nthawi yomweyo anasiya kutaya magazi.+
5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba+ timene amavala monga zodzitetezera, ndipo amakulitsanso ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa zovala zawo.
44 Mayiyu anamudzera kumbuyo Yesu n’kugwira ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa malaya ake akunja.+ Nthawi yomweyo anasiya kutaya magazi.+