Miyambo 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa cha kudzikuza, munthu amangoyambitsa mavuto,+ koma anthu amene amakhala pamodzi n’kumakambirana amakhala ndi nzeru.+ Afilipi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+
10 Chifukwa cha kudzikuza, munthu amangoyambitsa mavuto,+ koma anthu amene amakhala pamodzi n’kumakambirana amakhala ndi nzeru.+
3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+