1 Samueli 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+ Yuda 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale zili choncho, anthu amenewanso, pokonda zongolota,+ akuipitsa matupi ndi kunyalanyaza ulamuliro+ ndipo amalankhula zonyoza amene ali ndi ulemerero.+
23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+
8 Ngakhale zili choncho, anthu amenewanso, pokonda zongolota,+ akuipitsa matupi ndi kunyalanyaza ulamuliro+ ndipo amalankhula zonyoza amene ali ndi ulemerero.+