Yuda 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+
11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+