Numeri 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pa nthawi yosamutsa chihema chopatulika, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, iwo ndiwo azimanga chihemacho. Aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+ Numeri 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azikhala pafupi nanu kuti azichita utumiki wawo wonse wa pachihema chokumanako, ndipo munthu wina aliyense amene si Mlevi asayandikire kwa inu.+
51 Pa nthawi yosamutsa chihema chopatulika, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, iwo ndiwo azimanga chihemacho. Aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+
4 Azikhala pafupi nanu kuti azichita utumiki wawo wonse wa pachihema chokumanako, ndipo munthu wina aliyense amene si Mlevi asayandikire kwa inu.+