Levitiko 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu akapanga lonjezo lapadera+ lopereka munthu mnzake kwa Yehova pa mtengo woikidwiratu, Levitiko 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati msinkhu wa munthuyo ndi wapakati pa mwezi umodzi ndi zaka zisanu, akakhala wamwamuna mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli asiliva asanu,+ ndipo akakhala wamkazi ndi masekeli asiliva atatu.
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu akapanga lonjezo lapadera+ lopereka munthu mnzake kwa Yehova pa mtengo woikidwiratu,
6 Ngati msinkhu wa munthuyo ndi wapakati pa mwezi umodzi ndi zaka zisanu, akakhala wamwamuna mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli asiliva asanu,+ ndipo akakhala wamkazi ndi masekeli asiliva atatu.