Ekisodo 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kenako utenge nganga ya nkhosa yolongera Aroni unsembe,+ ndi kuiweyulira uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo ikhale gawo lako. Levitiko 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno wansembe azitentha mafutawo+ paguwa lansembe, koma ngangayo izikhala ya Aroni ndi ana ake.+ Levitiko 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nganga ya nsembe yoweyula+ ndiponso mwendo, umene ndi gawo lopatulika, ndikuzitenga pansembe zachiyanjano za ana a Isiraeli. Ndikuzitenga kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Ili ndi lamulo mpaka kalekale.
26 “Kenako utenge nganga ya nkhosa yolongera Aroni unsembe,+ ndi kuiweyulira uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo ikhale gawo lako.
31 Ndiyeno wansembe azitentha mafutawo+ paguwa lansembe, koma ngangayo izikhala ya Aroni ndi ana ake.+
34 Nganga ya nsembe yoweyula+ ndiponso mwendo, umene ndi gawo lopatulika, ndikuzitenga pansembe zachiyanjano za ana a Isiraeli. Ndikuzitenga kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Ili ndi lamulo mpaka kalekale.