Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Mlandu wofuna chigamulo ukakukulira kwambiri,+ monga mlandu wokhudza kukhetsa magazi,+ mlandu umene munthu wakasuma,+ mlandu wokhudza zachiwawa kapena mkangano+ umene wachitika mumzinda wanu, pamenepo uzinyamuka ndi kupita kumalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+

  • Yoswa 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Azithawira+ kumzinda umodzi mwa mizindayi n’kukaima pachipata+ cholowera mumzindawo. Akatero azifotokoza nkhani yake kwa akulu+ a mzindawo. Akuluwo amulandire n’kumupatsa malo mumzindamo kuti azikhala nawo limodzi.

  • 2 Mbiri 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa mlandu uliwonse wobwera kwa inu kuchokera kwa abale anu amene akukhala m’mizinda yawo, wokhudza kukhetsa magazi,+ chilamulo,+ ndi zigamulo,+ muziwachenjeza kuti asalakwire Yehova kuopera kuti mkwiyo wa Mulungu+ ungakuyakireni inuyo ndi abale anu. Muzichita zimenezi n’cholinga choti musapalamule mlandu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena