Deuteronomo 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Wotembereredwa ndi munthu wosuntha chizindikiro cha malire a mnzake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Yobu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pali anthu amene amasuntha malire,+Iwo alanda gulu la ziweto kuti aziziweta. Miyambo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usasunthire kumbuyo malire akalekale,+ ndipo usalowe m’munda mwa ana amasiye.*+
17 “‘Wotembereredwa ndi munthu wosuntha chizindikiro cha malire a mnzake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)