Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Mose anatumiza amunawo kunkhondo, amuna 1,000 pa fuko lililonse. Anawatumiza limodzi ndi Pinihasi,+ mwana wa wansembe Eleazara. Pinihasi ananyamula ziwiya zopatulika ndi malipenga+ operekera zizindikiro.

  • Oweruza 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Masiku amenewo Pinihasi,+ mwana wa Eleazara, mwana wa Aroni, ndiye anali kuimirira pafupi ndi likasalo.+ Chotero iye anafunsa kuti: “Kodi ndipitenso kukamenyana ndi ana a m’bale wanga Benjamini kapena ndisapite?”+ Poyankha, Yehova anati: “Pita, chifukwa mawa ndim’pereka m’dzanja lako.”+

  • 1 Samueli 30:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, Davide anauza Abiyatara+ wansembe, mwana wa Ahimeleki kuti: “Chonde, bweretsa efodi+ kuno.” Pamenepo Abiyatara anapereka efodi kwa Davide.

  • 2 Mbiri 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Taonani, ife patsogolo pathu pali Mulungu woona+ ndi ansembe ake,+ ndi malipenga+ otiitanira ku nkhondo yomenyana nanu. Inu ana a Isiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu,+ chifukwa simupambana.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena