Yoswa 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anawauza kuti: “Bwererani kumahema anu ndi chuma chambiri ndiponso ziweto zambiri, ndi siliva, golide, mkuwa, zitsulo, ndi zovala zambiri.+ Tengani katundu amene munafunkha+ kwa adani anu n’kugawana ndi abale anu.”
8 Anawauza kuti: “Bwererani kumahema anu ndi chuma chambiri ndiponso ziweto zambiri, ndi siliva, golide, mkuwa, zitsulo, ndi zovala zambiri.+ Tengani katundu amene munafunkha+ kwa adani anu n’kugawana ndi abale anu.”