2 Samueli 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Davide atamva zimenezi pambuyo pake, ananena kuti: “Pamaso pa Yehova, ineyo ndi ufumu wanga, mlandu wa magazi+ a Abineri mwana wa Nera sukutikhudza mpaka kalekale.* Salimo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita cholakwa chilichonse,+Ngati manja anga achita zosalungama zilizonse,+
28 Davide atamva zimenezi pambuyo pake, ananena kuti: “Pamaso pa Yehova, ineyo ndi ufumu wanga, mlandu wa magazi+ a Abineri mwana wa Nera sukutikhudza mpaka kalekale.*
3 Inu Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita cholakwa chilichonse,+Ngati manja anga achita zosalungama zilizonse,+