Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 29:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yakobo anagwira ntchito zaka 7 kuti atenge Rakele.+ Koma iye anangoziona zakazo ngati masiku ochepa chabe, chifukwa anam’konda kwambiri mtsikanayo.+

  • Genesis 34:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atatero, nthawi zonse mtima wake unali kulakalaka Dina mwana wa Yakobo, ndipo anamukonda kwambiri m’tsikanayu, moti ankalankhula naye momunyengerera.

  • Oweruza 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako anapita kukauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ine ndaona mkazi ku Timuna mwa ana aakazi a Afilisiti, choncho mukam’tenge kuti akhale mkazi wanga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena