Levitiko 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo akapolowa muzisiyira ana anu monga cholowa chawo mpaka kalekale.+ Amenewa ndiwo azikhala akapolo* anu, koma abale anu, ana a Isiraeli, musawapondereze ndi kuwachitira nkhanza.+
46 Ndipo akapolowa muzisiyira ana anu monga cholowa chawo mpaka kalekale.+ Amenewa ndiwo azikhala akapolo* anu, koma abale anu, ana a Isiraeli, musawapondereze ndi kuwachitira nkhanza.+