Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 M’mwezi wachitatu kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo,+ pa tsiku lomwelo,* iwo analowa m’chipululu cha Sinai.+

  • Numeri 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano m’chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, pa tsiku la 20,+ mtambo uja unanyamuka pamwamba pa chihema+ cha Umboni.

  • Numeri 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Nawonso ana a Isiraeli ananyamuka mwa dongosolo lawo lonyamukira.+ Ananyamuka m’chipululu cha Sinai, ndipo mtambowo unakaima m’chipululu cha Parana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena