Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Usadane ndi m’bale wako mumtima mwako.+ Mnzako um’dzudzule ndithu+ kuti usasenze naye tchimo. Deuteronomo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Mwamuna akatenga mkazi ndi kugona naye koma sakum’kondanso,+