Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 38:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako anachita chiwerewere,+ ndipo ali ndi pakati.”+ Yuda atamva zimenezo, anati: “M’tulutseni kuti aphedwe ndi kuotchedwa.”+

  • Deuteronomo 22:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 azim’bweretsa mtsikanayo pakhomo la nyumba ya bambo ake ndipo amuna a mumzindawo azim’ponya miyala kuti afe, chifukwa wachita chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli,+ mwa kuchita uhule m’nyumba ya bambo ake.+ Motero muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • Salimo 141:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Musachititse mtima wanga kukonda choipa chilichonse,+

      Kuti ndisamachite zinthu zoipa zonditchukitsa,+

      Pamodzi ndi amene amachita zinthu zopweteka anzawo,+

      Kuti ndisadye chakudya chawo chapamwamba.+

  • Hoseya 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulankhula kudzera mwa Hoseya, ndipo Yehova anauza Hoseya kuti: “Pita+ ukakwatire mkazi amene adzachita dama. Pamenepo udzakhala ndi ana chifukwa cha dama la mkazi wakoyo. Pakuti mwanjira yofanana ndi zimenezi, dzikoli latembenuka ndi kusiya kutsatira Yehova chifukwa cha dama.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena