Levitiko 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘Muzionetsetsa kuti ana a Isiraeli akupewa choipitsa chilichonse, kuopera kuti angafe chifukwa choipitsa chihema changa chopatulika chimene chili pakati pawo.+
31 “‘Muzionetsetsa kuti ana a Isiraeli akupewa choipitsa chilichonse, kuopera kuti angafe chifukwa choipitsa chihema changa chopatulika chimene chili pakati pawo.+