Deuteronomo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova Mulungu wako adzakudalitsa ndithu monga mmene anakulonjezera ndipo mitundu yambiri idzakongola+ zinthu zako mwa kukupatsa chikole, pamene iwe sudzakongola kanthu. Udzalamulira mitundu yambiri koma mitundu sidzakulamulira.+
6 Yehova Mulungu wako adzakudalitsa ndithu monga mmene anakulonjezera ndipo mitundu yambiri idzakongola+ zinthu zako mwa kukupatsa chikole, pamene iwe sudzakongola kanthu. Udzalamulira mitundu yambiri koma mitundu sidzakulamulira.+