Miyambo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu amene amachulukitsa zinthu zamtengo wapatali kuchokera ku chiwongoladzanja ndi katapira,*+ amangosungira zinthuzo munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+ Ezekieli 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye sapondereza munthu wosautsika. Sakongoza zinthu mwa katapira+ ndipo salandira chiwongoladzanja.+ Amatsatira zigamulo zanga+ ndi kuyenda motsatira malamulo anga.+ Munthu wotere sadzafa chifukwa cha zolakwa za bambo ake.+ Adzakhalabe ndi moyo.+
8 Munthu amene amachulukitsa zinthu zamtengo wapatali kuchokera ku chiwongoladzanja ndi katapira,*+ amangosungira zinthuzo munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+
17 Iye sapondereza munthu wosautsika. Sakongoza zinthu mwa katapira+ ndipo salandira chiwongoladzanja.+ Amatsatira zigamulo zanga+ ndi kuyenda motsatira malamulo anga.+ Munthu wotere sadzafa chifukwa cha zolakwa za bambo ake.+ Adzakhalabe ndi moyo.+