Deuteronomo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi pali amene analonjeza mkazi kuti adzamukwatira ndipo sanamutenge? Achoke ndi kubwerera kunyumba yake,+ kuopera kuti angafe pankhondo ndipo mwamuna wina angatenge mkaziyo.’ Luka 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komanso wina anati, ‘Ine ndangokwatira kumene,+ choncho sindingathe kubwera.’
7 Kodi pali amene analonjeza mkazi kuti adzamukwatira ndipo sanamutenge? Achoke ndi kubwerera kunyumba yake,+ kuopera kuti angafe pankhondo ndipo mwamuna wina angatenge mkaziyo.’