Deuteronomo 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 muziichitira zimene inafuna kuti zichitikire m’bale wakezo,+ ndipo muzichotsa woipayo pakati panu.+ Deuteronomo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wawo azim’ponya miyala ndi kumupha. Muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha kwambiri.+
19 muziichitira zimene inafuna kuti zichitikire m’bale wakezo,+ ndipo muzichotsa woipayo pakati panu.+
21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wawo azim’ponya miyala ndi kumupha. Muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha kwambiri.+