Yobu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Oipa amalanda mwana wamasiye kum’chotsa pabere.+Amatenga ngati chikole chovala chimene wozunzika wavala.+ Yobu 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ozunzika amayenda opanda chovala,Amasenza mitolo ya tirigu ali ndi njala.+
9 Oipa amalanda mwana wamasiye kum’chotsa pabere.+Amatenga ngati chikole chovala chimene wozunzika wavala.+