Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama. Deuteronomo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzipita kwa ansembe+ achilevi ndi kwa woweruza+ amene aziweruza m’masiku amenewo. Uziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuza chigamulo.+
18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.
9 Uzipita kwa ansembe+ achilevi ndi kwa woweruza+ amene aziweruza m’masiku amenewo. Uziwafotokozera nkhaniyo ndipo iwo azikuuza chigamulo.+