Levitiko 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 wanundu, woonda,* wa diso lamatenda, wa nkhanambo, wa zipere kapena wotswanyika mavalo.+ Deuteronomo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Mwamuna wofulidwa+ mwa kuphwanya mavalo+ ake kapena woduka maliseche asalowe mumpingo wa Yehova.