Ekisodo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, ndamva kulira kwa ana a Isiraeli, komanso ndaona kupondereza kumene Aiguputo akuwapondereza.+ Salimo 116:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 116 Mtima wanga ndi wodzaza ndi chikondi, chifukwa Yehova amamva+Mawu anga ndi madandaulo anga.+
9 Taona, ndamva kulira kwa ana a Isiraeli, komanso ndaona kupondereza kumene Aiguputo akuwapondereza.+