Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 102:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iye wayang’ana pansi ali kumalo oyera, okwezeka,+

      Yehova wayang’ana dziko lapansi ali kumwambako,+

  • Yesaya 40:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pali Winawake amene amakhala pamwamba pa dziko lapansi lozungulira,+ limene okhalamo ake ali ngati ziwala. Iye anayala kumwamba ngati nsalu yopyapyala, ndipo anakutambasula ngati hema wokhalamo.+

  • Yesaya 63:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yang’anani muli kumwamba,+ ndipo muone kuchokera pamalo anu okhala apamwamba, oyera ndi okongola.+ Kodi mtima wanu wodzipereka kwambiri+ ndiponso mphamvu zanu zonse zili kuti? Kodi kubwadamuka kwa m’mimba mwanu+ ndi chifundo+ chanu zili kuti? Inuyo mwaleka kundichitira zimenezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena