Deuteronomo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu. Deuteronomo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu. Deuteronomo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake.
4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu.
6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu.
11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake.