Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+

  • 1 Mafumu 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uzimvera Yehova Mulungu wako mwa kuyenda m’njira zake,+ kusunga malamulo ake, zigamulo zake,+ ndi maumboni* ake, malinga ndi zimene zinalembedwa m’chilamulo cha Mose.+ Uzitero kuti udzakhale wanzeru m’zochita zako zonse, ndiponso kulikonse kumene udzapite.

  • Mateyu 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye anamuyankha kuti: “N’chifukwa chiyani ukundifunsa chimene chili chabwino? Pali Mmodzi yekha amene ali wabwino.+ Chotero ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+

  • 1 Yohane 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena