Deuteronomo 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Ndiyeno Yehova Mulungu wanu akadzakulowetsani m’dziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu,+ mukatchule dalitsoli paphiri la Gerizimu+ ndipo temberero mukalitchulire paphiri la Ebala.+
29 “Ndiyeno Yehova Mulungu wanu akadzakulowetsani m’dziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu,+ mukatchule dalitsoli paphiri la Gerizimu+ ndipo temberero mukalitchulire paphiri la Ebala.+