Levitiko 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Usavule mkazi wa bambo ako,+ chifukwa kumeneko n’kuvula bambo ako. 2 Samueli 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho anamangira Abisalomu hema padenga,+ ndipo Abisalomu anayamba kugona ndi adzakazi a bambo ake,+ Aisiraeli onse akuona.+ 1 Akorinto 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mbiri yamvekatu kuti pakuchitika dama*+ pakati panu, ndipo dama lake ndi loti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+
22 Choncho anamangira Abisalomu hema padenga,+ ndipo Abisalomu anayamba kugona ndi adzakazi a bambo ake,+ Aisiraeli onse akuona.+
5 Mbiri yamvekatu kuti pakuchitika dama*+ pakati panu, ndipo dama lake ndi loti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+