Ekisodo 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Aliyense wogonana ndi nyama aziphedwa ndithu.+ Levitiko 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Usagone ndi nyama iliyonse*+ n’kukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kumeneko n’kuchita zosemphana ndi chibadwa. Levitiko 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Mwamuna akagona ndi nyama,*+ aziphedwa ndithu ndipo muziphanso nyamayo.
23 “‘Usagone ndi nyama iliyonse*+ n’kukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kumeneko n’kuchita zosemphana ndi chibadwa.