Levitiko 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Deuteronomo 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke+ ndipo musapatuke ndi kupembedza milungu ina n’kumaiweramira.+ Salimo 96:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+ 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke+ ndipo musapatuke ndi kupembedza milungu ina n’kumaiweramira.+
5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+