Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+ Yeremiya 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+
48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+
6 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+