Genesis 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+ Ekisodo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+ Salimo 105:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wakumbukira pangano limene anapangana ndi Abulahamu,+Ndi lonjezo limene analumbira kwa Isaki,+
3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+
24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+