Ekisodo 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anali kugulula mawilo a magaleta awo moti anali kuwayendetsa movutikira.+ Pamenepo Aiguputo anayamba kunena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+ 1 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+
25 Iye anali kugulula mawilo a magaleta awo moti anali kuwayendetsa movutikira.+ Pamenepo Aiguputo anayamba kunena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+
2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+