Salimo 68:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali m’magulu a masauzande makumimakumi, ali m’magulu a masauzande osawerengeka.+Yehova walowa m’malo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+
17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali m’magulu a masauzande makumimakumi, ali m’magulu a masauzande osawerengeka.+Yehova walowa m’malo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+