Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+ Machitidwe 7:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 inu amene munalandira Chilamulo kudzera mwa angelo,+ koma osachisunga.”
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+