Yoswa 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ana a Isiraeli sanapitikitse+ Agesuri ndi Amaakati. Ndipo iwo+ akukhalabe pakati pawo kufikira lero. 2 Samueli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wake wachiwiri anali Kileyabu+ wobadwa kwa Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala, ndipo wachitatu anali Abisalomu+ wobadwa kwa Maaka, mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya ku Gesuri.
13 Koma ana a Isiraeli sanapitikitse+ Agesuri ndi Amaakati. Ndipo iwo+ akukhalabe pakati pawo kufikira lero.
3 Mwana wake wachiwiri anali Kileyabu+ wobadwa kwa Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala, ndipo wachitatu anali Abisalomu+ wobadwa kwa Maaka, mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya ku Gesuri.