2 Mbiri 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Masiku ambiri Aisiraeli+ anakhala opanda Mulungu woona, opanda wansembe woti aziwaphunzitsa+ ndiponso opanda Chilamulo. 2 Mbiri 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anayamba kuphunzitsa+ mu Yuda pogwiritsira ntchito buku la chilamulo cha Yehova.+ Ankayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda n’kumaphunzitsa anthu. Malaki 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+
3 Masiku ambiri Aisiraeli+ anakhala opanda Mulungu woona, opanda wansembe woti aziwaphunzitsa+ ndiponso opanda Chilamulo.
9 Iwo anayamba kuphunzitsa+ mu Yuda pogwiritsira ntchito buku la chilamulo cha Yehova.+ Ankayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda n’kumaphunzitsa anthu.
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+