Genesis 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+ 1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+
7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+
2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+