Ekisodo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ine ndikudziwa bwino kuti mfumu ya Iguputo sidzakulolani kupita kufikira nditaisonyeza mphamvu zanga.+ Deuteronomo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamapeto pake Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu+ ndi mkono wotambasula,+ zoopsa zazikulu,+ zizindikiro ndi zozizwitsa.+ Luka 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zotani?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri+ wamphamvu m’ntchito ndi m’mawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.
19 Koma ine ndikudziwa bwino kuti mfumu ya Iguputo sidzakulolani kupita kufikira nditaisonyeza mphamvu zanga.+
8 Pamapeto pake Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu+ ndi mkono wotambasula,+ zoopsa zazikulu,+ zizindikiro ndi zozizwitsa.+
19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zotani?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri+ wamphamvu m’ntchito ndi m’mawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.