Miyambo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Lidzakutsogolera ukamayenda,+ lidzakulondera ukamagona,+ ndipo ukadzuka, lidzakusamalira.