Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+ Deuteronomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+
18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+
11 “Choncho anthu inu munayandikira ndi kuimirira m’munsi mwa phiri. Phiri limenelo linali kuyaka moto mpaka kumwamba, ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+