Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamenepo Aiguputo anawalondola, ndipo mahatchi onse a Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi, anayamba kuwathamangira,+ kulowa pakati pa nyanja.

  • Salimo 136:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Amenenso anakutumulira Farao ndi gulu lake lankhondo m’Nyanja Yofiira:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Aheberi 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena